Utumiki:Part 23 (A)

Mulungu povumbulutsa Muhammad (s.a.w.w) kukhala Mtumiki adapereka mtendere waukulu kwa mtundu wa anthu kuti achoke mu umbuli ndi kuponderezedwa. Mtumiki ndi ntchito yake yaikulu yomwe adaigwira adakwanitsa kuchotsa anthu muzinthu zabodza, uchinyama ndikwabweretsera mtendere ndi umoyo wabwino.

AttachmentSize
File e13b2845d6d59eb2a3a86d1105667223.mp414.12 MB

Add new comment