Tawassul mu Quran ndi riwayat:Part 2

Mulungu adati: “E! Adam, wamudziwa bwanji Muhammad poti ine sindidamulenge?” Adayankha: “ Nthawi yomwe mudandilenga ndidayang’ana kuchimpando chanu chaufumu ndipo ndidaona kutalembedwa mau oti: Palibe Mulungu ompembedza mwachoonadi koma Mulungu mmodzi yek

Mulungu adati: “E! Adam, wamudziwa bwanji Muhammad poti ine sindidamulenge?” Adayankha: “ Nthawi yomwe mudandilenga ndidayang’ana kuchimpando chanu chaufumu ndipo ndidaona kutalembedwa mau oti: Palibe Mulungu ompembedza mwachoonadi koma Mulungu mmodzi yekha ndipo Muhammad ndi Mthenga wa Mulungu...

AttachmentSize
File 12106-f-chichwa.mp447.81 MB