Zionetsero za Husain(a) mu Quran 5

Zionetsero za Husain(a) mu Quran 5

 
 Mulungu akunena  kuti:
و إذا الموئودة سئلت * بأى ذنب قتلت   التكوير / 8 - 9
Nthawi  yomwe  ana  achikazi  omwe  amaikidwa  mmanda  amoyo  adzafunsidwa  kuti  ndichifukwa  chani  adaphedwa?
Imam  Swadiq (a)  adanena  kuti  aya  imeneyi  idatsikira  Imam  Husain (a).
Al’awalim,volume 15, tsamba 19.