Zionetsero za Husain (a) mu Quran 3

Zionetsero za Husain (a) mu Quran 3

((و لا تقتلوا النفس التى حرم الله الا بالحق))  (الاسراء / 33) 

  Mulungu  akunena  kuti ((Musamuphe  munthu  yemwe  ali  oletsedwa  kuphedwa  pokha pokha  ngati  pali  chilungamo  choti aphedwe)).
Imam  Swadiq (a)  adanena  kuti  tanthauzo  la  munthu  yemwe  ali  oletsedwa  kuphedwa  ndi Husain  yemwe  adamupha   pakati pa banja  lake.