فیلم

Quran, Sunnah, Din, Religion, Wahabism, Sunni, chishia, Shia, Shiism, chisilamu, Islam, Wahabiyyat, nkhani, Ahal bait, Wahabism, Azodori.
Pankhani yakubwera kwa Mahdi mashia ndi Ahlu sunnat ndiogwirizana maganizo angakhalenso amene sali asilamu za Imam ameneyu zidalembedwa mmabuku awo kuti kumapeto kwa dziko kudzabwera mpulumutsi.
Quran, Sunnah, Din, Religion, Wahabism, Sunni, chishia
Imam Mahdi (a.s) asadabwere padzakhala zinonetsero zakubwera kwake ndipo zionetsero zimenezi zili za mitundu iwiri: a- Zionetsero zakumayambiriro kwa kubwera kwake. b- Zionetsero zotsimikiza kubwera kwake ( zikaoneka zimenezo ndiye kuti nthawi yakubwera
Sunnah, Din, Religion, Wahabism, Sunni, chishia,
Mulungu adati: “E! Adam, wamudziwa bwanji Muhammad poti ine sindidamulenge?” Adayankha: “ Nthawi yomwe mudandilenga ndidayang’ana kuchimpando chanu chaufumu ndipo ndidaona kutalembedwa mau oti: Palibe Mulungu ompembedza mwachoonadi koma Mulungu mmodzi yek

Pages