فیلم

Mukuyang’ana kwa mashia akunena kuti Mtumiki wawo Muhammad (s.a.w.w) ndi yemweyo yemwe Ahlusunnah ali nawo. Kusonyeza kuti Mtumiki wawo onsewa ndi Muhammad bin Abdullah.
Utumiki:Gawo 25 (B)
Mipatuko iwiri imeneyi (Shia ndi Sunni) ndiofanana muzikhulupiriro zokhudza Mtumiki (s.a.w.w). Onse amakhulupirira kuti Mtumiki ndi: - otumizidwa ndi Mulungu. - Mtumiki omaliza. - Munthu osankhidwa ndi Mulungu kudzaongola anthu.
Kusiyana kwa Chiwahhabi ndi Sunni:Gawo1
Ahlusunnat ali a mipatuko inayi:1- Hannafi 2- Hanbali 3 –Shafi ndi Maliki. Kuchokera mmipatuko imeneyi pakupezekanso mipatuko ina ing’ono ing’ono yomwe ikuchokera mmenemu monga mmpatuko wa chiwahhabi omwe umazinena kuti umatsatira zikhulupiriro za Hanbal
Kusiyana kwa Chiwahhabi ndi Sunni:Gawo 2
Maulawi Abdulrahim (sunni) akunena kuti: “Pakati pa mawahhabi ndi sunni pali kusiyana kwambiri pakuganiza ndizikhulupiriro....Mau anga kwa asilamu asunni anzanga ndi oti mpatuko wachiwahhabi ndiosochera ndipo ukufuna kuononga chisunni choncho musanyengeke
Chiwahhabi mukuyang’ana kwa Sunni:Gawo 2
Shaikh wapa Azhar adanena kuti: Mubarrak pofuna kusangalatsa Zionists adali kutilimbikitsa kuti tizigwiritsa ntchito mafatwa achiwahhabi osochera ndikumazetsa kusiyana maganizo pakati pa asilamu ndi mipatuko yawo monga asunni ndi mashia.

Pages