فیلم

Quran, Sunnah, Din, Religion, Wahabism, Sunni, chishia,
Kupempha chithandizo kwa Mulungu kudzera mwa Atumiki ndi anthu oyera sizikutanthauza kuti anthu amenewa tikuwayika pamalo ofanana ndi Mulungu ayi, koma kuti chifukwa cha ulemelero ndiupamwamba komanso kuyandikira kwa iwowo kwa Mulungu...
Quran, Sunnah, Din, Religion, Wahabism, Sunni, chishia,
Munthu amene waikira umboni za umodzi wa Mulungu ndi utumiki wa Muhammad ndinso ndikuimika mapemphero, kupereka chopereka, kusala chakudya mmwezi wa Ramadhan ndikupita ku hajji ndi msilamu choncho chuma chake, moyo wake abale ake ndizotetezedwa komanso n
Quran, Sunnah, Din, Religion, Wahabism, Sunni, chishia,
Muchisilamu muli nkhani yoti msilamu wina aliyense ali ndi ufulu (Haqq) kwa msilamu nzake. Angakhale zinyamanso zili ndi ufulu kwa munthu mwachitsanzo ngati munthu ali ndi chinyama chomwe amachigwiritsa ntchito kaya yolima kapena kukwera adziwe kuti....
Quran, Sunnah, Din, Religion, Wahabism, Sunni, chishia,
Monga momwe tidalongosolera kukumana kwadutsa pankhani ya mapata achipembedzo cha chisilamu kuti ndi kukhulupirira za umodzi wa Mulungu, Utumiki wa Muhammad ndi Kuuka kwa akufa.
Quran, Sunnah, Din, Religion, Wahabism, Sunni, chishia, Shia, Shiism, chisilamu, Islam, Wahabiyyat, nkhani, Ahal bait, Wahabism, Azodori.
Mulungu povumbulutsa Muhammad (s.a.w.w) kukhala Mtumiki adapereka mtendere waukulu kwa mtundu wa anthu kuti achoke mu umbuli ndi kuponderezedwa. Mtumiki ndi ntchito yake yaikulu yomwe adaigwira adakwanitsa kuchotsa anthu muzinthu zabodza, uchinyama ndikwa
Hz;Nuh (as)’ın,Kısaca, Hayatını, Kur’an, ışığında, anlatmaya, çaılışarak , o ,dönemdeki, toplumsal ,sıkıntıları, tahlil ,ederek ,bu ,dönemdeki ,toplumun yaşadıklarına, benzerlik, yönlerinide ,ele, aldık.
Hz;Nuh (as)’ın Kısaca Hayatını Kur’an ışığında anlatmaya çaılışarak o dönemdeki toplumsal sıkıntıları tahlil ederek bu dönemdeki toplumun yaşadıklarına benzerlik yönlerinide ele aldık.
Quran, Sunnah, Din, Religion, Wahabism, Sunni, chishia, Shia, Shiism, chisilamu, Islam, Wahabiyyat, nkhani, Ahal bait, Wahabiyyat, Wahabisim, Azodori.
Liu lotiأمّيّ muchiluya likuchokera pa mau awiri أمّ (mai) kapena أمّة (Gulu). Anthu otanthauzira Quran adati Ummiyy kutanthauza kusawerenga monga momwe adabadwira mwa mai ake ndipo sadapite kusukulu.
Quran, Sunnah, Din, Religion, Wahabism, Sunni, chishia, Shia, Shiism, chisilamu, Islam, Wahabiyyat, nkhani, Ahal bait, Wahabism, Azodori.
“ Ngati utsogoleri wadziko lapansi udakapatsidwa mmanja mwa Muhammad, dziko lapansi lidakakhala pachisangalalo. Chisilamu chidakatsogolera dziko lonse ku kupambana ndikuthetsa mavuto onse.”
Quran, Sunnah, Din, Religion, Wahabism, Sunni, chishia, Shia, Shiism, chisilamu, Islam, Wahabiyyat, nkhani, Ahal bait, Wahabism, Azodori.
Kodi zikhulupiriro zimenezi ndizoona? Mtumiki yemwe Mulungu akumutcha kuti Rahmatulilialamina, oti kungo mwalira alibenso phindu? Ndichifukwa chiyani ife mu athana pambuyo pakuvomereza ndikuikira umboni za umodzi waMulungu tiyenera kuikiranso umboni za Mu
Quran, Sunnah, Din, Religion, Wahabism, Sunni, chishia, Shia, Shiism, chisilamu, Islam, Wahabiyyat, nkhani, Ahal bait, Wahabism, Azodori.
Muhammad Abdul Wahhabi adanena mubukhu lake la Tauhid kuti kupereka dzina la Abdul posakhala Mulungu ndi shrik, pachifukwachi iye adanena kuti Hazrat Adam ndi mkazi wake ndi mamushrik chifukwa choti adapereka dzina la Abdul harith kwa mwana wawo.
Quran, Sunnah, Din, Religion, Wahabism, Sunni, chishia, Shia, Shiism, chisilamu, Islam, Wahabiyyat, nkhani, Ahal bait, Wahabism, Azodori.
Fatima ndi mwana wa Mtumiki (s.a.w.w). Iye ali maina opatsidwa (laqab) ambiri monga: Zahra, Maridhiyya, Batuli, Muhditha ...
Quran, Sunnah, Din, Religion, Wahabism, Sunni, chishia, Shia, Shiism, chisilamu, Islam, Wahabiyyat, nkhani, Ahal bait, Wahabism, Azodori.
Fatima ndi mwana wa Mtumiki (s.a.w.w). Iye ali maina opatsidwa (laqab) ambiri monga: Zahra, Maridhiyya, Batuli, Muhditha.Tikafuna kukamba za upamwamba wake pamaso pa bambo ake (s.a.w.w) kwakwana kunena kuti:..
Quran, Sunnah, Din, Religion, Wahabism, Sunni, chishia, Shia, Shiism, chisilamu, Islam, Wahabiyyat, nkhani, Ahal bait, Wahabiyyat, Wahabisim, Azodori.
Ma wahhabi su’udi mchaka cha 1220 kapena 1221 adachita chiwembu nzinda wa Madina ndipo adauzungulira kwa chaka chimodzi ndi theka ndipo mapeto ake nzindawu udakhala mmanja mwawo.
 Quran, Sunnah, Din, Religion, Wahabism, Sunni, chishia, Shia, Shiism, chisilamu, Islam, Wahabiyyat, nkhani, Ahal bait, Wahabiyyat, Wahabisim, Azodori.
Ma wahhabi su’udi mchaka cha 1220 kapena 1221 adachita chiwembu nzinda wa Madina ndipo adauzungulira kwa chaka chimodzi ndi theka ndipo mapeto ake nzindawu udakhala mmanja mwawo.
Quran, Sunnah, Din, Religion, Wahabism, Sunni, chishia, Shia, Shiism, chisilamu, Islam, Wahabiyyat, nkhani, Ahal bait, Wahabism, Azodori.
Iye azamenya nkhondo ndi adani ake komanso otsutsana naye. Chifukwa choti pazapezeka magulu ena omwe sadzagwirizana ndizomwe azidzalalikira ndikuitanira iye komanso kukhazikitsa kwake chilungamo.
Quran, Sunnah, Din, Religion, Wahabism, Sunni, chishia, Shia, Shiism, chisilamu, Islam, Wahabiyyat, nkhani, Ahal bait, Wahabism, Azodori.
Mtumiki adanena kuti nthawi ya Imam Zaman umoyo wudzakhala wapamwamba kuposa nyengo zonse ndipo chuma chidzapita patsogolo komanso nthaka sidzasiya kanthu osakameretsa.

Pages