Chikhirisitu chenicheni ndi chiti? 1

Ngati mkhirisitu angalowe chisilamu, sizikutanthauza kuti adzatalikirana ndi olemekezeka mzimu wa Mulungu, liwu la Mulungu komanso mtumiki wa Mulungu Yesu (mtendere ndi madalitso a Mulungu apite kwa iye) ndinso mayi ake olemekezeka mayi Maria yemwe ali bwana wa amayi komanso mboni ya Mulungu kwa amayi adziko lapansi. Koma kuti ndipomwe kuzindikira kwake kudzawonjezereka, azadziwa zowonadi za anthu amenewa, ulemelero wawo komanso chikondi chawo kwa iwo chidzapita patsogolo komanso chidzawonjezereka

AttachmentSize
File 6917e5d76a49b33190ec80791483604f.mp417.08 MB