Ziyarat Ashura Part 3

Mtumiki adalankhula Hadith ina kuti: "Husein ndi ochokera mwa ine ndipo ine ndi ochokera mwa Husein, Mulungu amukondo yemwe adzamukonda iye ndipo Mulungu adane naye yemwe adzadana ndi Husein". Adani ena atawona kuti sadatengepo gawo pomupha Imam Husein (a.s) adatenga ndodo ndikumamenya pakamwa ndi mutu wake ndikumati ifenso tipeze nawo zabwino (Thawab) pomupha mwana wa mtumikiyu…

AttachmentSize
File 15f9768904cb2e6f97a9efa0677c2578.mp418.94 MB