Adaphedweranji Imam Husein (a.s) 4

Imam Ridha (a.s) akumuwuza Ibn Shabib yemwe adali m'modzi mwa omutsatira ake kuti: "Ngati wakumana ndi vuto lina lake kapena ukumva kuwawa ndi ululu kwambiri ndiye ukufuna kulira pavutolo, uyenera kumulilira Husein (a.s) mwachoncho vuto lako udzaliwona ngati sivuto chifukwa chakuti iye adazingidwa ngati momwe chimazingidwira chinyama" komanso iye ndi amene adakumana ndi vuto lalikulu ndinso lopweteka kwambiri kuposa lomwe munthu angakumane nalo mu umoyo watsiku ndi tsiku. Mavuto onse akusonkhana mwa Imam Husein (a.s).

AttachmentSize
File f45ec8c2663e9785f77b0342d6802c85.mp417.2 MB