Adaphedweranji Imam Husein (a.s) 2

Koma kulongosola zokhudzana ndi kumulilira Imam Husein (a.s) kwa munthu amene sadayike phazi lake munjira ya Imam Husein (a.s) ndi Ahalbait (a.s) zidzakhala ngati kulankhulana ndi munthu yemwe ali osawona komanso osamva. Kodi munthu yemwe ali osamva komanso osawona angamve chiyani pazomwe ungamuwuze? Mwachoncho munthu ameneyu mapeto ake adzalankhula zinthu zomwe zidzakhala zosemphana ndi chikhalidwe cha Quran komwe kuli kulira ngati momwe zikuwonekera m'ma Ayah ena.

AttachmentSize
File f56451d151c9154249d4b281f3af4b4e.mp422.18 MB

Add new comment