Ziyarat Ashura (1)

Ziyaarah ndi kupeleka Salamu kwa anthu iomwe adali osankhika ndi Mulungu ndi chikhalidwe cha Mulungu komanso Quran, mwachoncho munthu amene angatsutsane ndi zimenezi ndiye kuti akulimbana komanso akutsutsana ndi mchitidwe wa Mulungu ndi Quran komanso pang’ono pang’ono akutuluka muchipembedzo cha Mulungu chifukwa chakuti ngakhale mu Swalat mudayikidwa Ziyarah imeneyi pomwe ziri zokakamizidwa kwa munthu yemwe akupemphera kuti akafika pa Tashahud ayenera kupereka Salam kwa mtumiki ndi anthu opanga ntchito zabwino…

AttachmentSize
File 0aa09029fbb8dbd330e4d5a05a4ca189.mp423.7 MB

Add new comment