Imam Ridha (a.s) akufuna kutipulumutsa

Imam Redha (a.s) akuti: "Munthu yemwe adzamuyendera iye (kuwerenga ziyarah yake) kuchokera kutali (komwe munthuyo akukhala) , ndithudi adzamuteteza ndi kumugwira dzanja opanga ziyarayo patsiku la Qiyamah m'malo atatu, 1) nthawi yomwe mabukhu adzamwazidwa ndipo munthu adzazizwa kusowa chopanga, 2) pa bridge lowopsa lija (Sirat), 3) panthawi yomwe azidzayesa ntchito zake pa sikelo (Mizan).

AttachmentSize
File 8fbdd7d0c23ffb7643abaeef9620c51f.mp417.39 MB