Chiphunzitso cha Imam Ridha (a.s) mu umoyo wathu

Yemwe angamukonde munthu opanga tchimo, iyenso ndi watchimo. Yemwe angamukonde munthu opanga chilamulo cha Mulungu, iyenso adzakhala omvera chilamulo cha Mulungu (apeza thawab). Apa ndipomwe munthu akuyenera kusankha munthu yemwe adzakhala bwenzi lake. Munthu amene angamuwonelere opondereza osatengapo gawo potsutsa ndiye kuti iyenso ndi opondereza. Ndipo ngati angatengepo gawo potsutsa ndiye kuti iye ndi wachilungamo.

AttachmentSize
File 8c9190b0d51da0c018da4298ea09f272.mp413.51 MB