Ahalbait (A.S) ali ngati chombo cha mtumiki Nowa (A.S)

Ahalsunna akulephera kulongosola momveka bwino pokhudzana ndi Hadith yomwe mtumiki adanena kuti pambuyo pake padzabwera atsogoleri okwana khumi ndi awiri (12). Ndipo munthu akufunsa kuti kodi atsogoleri amenewa ndi ndani?

AttachmentSize
File 8971beeb41369acf68f79dde5f8890b1.mp425.31 MB