Kumudziwa Imam Sadiq (A.s) mwachidule (2)

Titha kuzindikira ulemelero wa Imam Sadiq (A.S) kudutsira mu zinthu zomwe adatisiyira ndi zomwe adalankhula pofuna kumugwira dzanja munthu ndikukamufikitsa kwa Mulungu. Monga Misbahu Alshariah pokhudzana ndi munthu yemwe akufuna kufika kwa Mulungu.

AttachmentSize
File 7c43f958f11c25b203899b44215df719.mp415.31 MB