Zolankhula za Imam Baqir (a.s) 6.

Imam Baqir (a.s) adanena kuti: من كان ظاهِرُه أرجَحَ من باطِنِه خَفَّ مِيزانُه. - Munthu yemwe angakongoletse maonekedwe ake akunja kuposa zobisika zake, sikelo yantchito zake idzakhala yopepuka tsiku lomaliza. Apa Imam akufuna kutiwuza kuti munthu ayenera kuwonetsetsa kuti ntchito zake zomwe amapanga mobisika ziyenera kukhala zabwino ndi zokongola osati kukhala ndimaonekedwe abwino koma ntchito zake ndikukhala zoipa.

AttachmentSize
File 0d115f703a77df248a63c00b6c868278.mp413.85 MB

Add new comment