Ndi chifukwa chiyani sindine mkhirisitu?-6

Kusamudziwa Mulungu ndi zomwe zidapangitsa kuti anthu ena amutenga Yesu kuti ndi Mulungu, akuti chifukwa chakuti Yesu amadzutsa akufa ndi kumalenga zinthu pozipanga kukhala za moyo kapena chifukwa chakuti adabadwa popanda bambo. Dziwani kuti Mulungu ali ndi mphamvu zoti akutha kulenga chinthu popanda bambo ndi mayi, popanda bambo keneko ndikuyika mphamvu mwa chinthu chimenechi ndikutha kumapanganso zinthu zina mumphamvu ya Mulunguyo, ngati momwe amapangira atumiki ena.

AttachmentSize
File e0ae49a38e326a6e1adc35330d7f4cf8.mp417.52 MB

Add new comment