Ndi chifukwa chiyani sindine mkhirisitu?- 5

Kupezeka kwa zikhulupiliro zina muchipembedzo cha Chikhirisitu – monga kukhulupilira za Milungu itatu (Trinity) – zidapangitsa kuti magulu ena akulu akulu achoke ndikupanga gulu lina posagwirizana ndi chikhulupiliro chimenechi. Dziwani kuti kumutenga Yesu kuti ndi Mulungu kapena mwana wa Mulungu, sizikutanthauza kuti mwamukweza Yesu koma kumenezu ndi kumutsitsa komanso kumunyoza Yesu. Choyamba yang\'anani ndi kudziwa kaye mbiri za Mulungu ndiye kenako muzamuyang\'ane Yesu kuti ndi zotheka munthu ameneyu kukhala Mulungu kapena mwana wa Mulungu.

AttachmentSize
File 8782234f22924559eb2d950cffb316a3.mp424.67 MB