Ndi chifukwa chiyani sindine mkhirisitu?- 4

Pakati pa akhirisitu pamalongosoledwa kuti Ana awiri akazi a Mtumiki Loti (A.S) adamwetsa bambo awo Mowa, mapeto ake ataledzera adagona nawo ndipo kuchokera mwa atsikana awiriwa mudabadwa ananso awiri, ndipo zimanenedwa kuti ana awiriwa ndi makolo (agogo) a olemekezeka Yesu (A.S). komanso akhirisitu amakhulupilira kuti panthawi yomwe Mayi Maria (S.A) adabadwitsa mwana, adali atafunsiridwa kale ndi mwamuna wina otchedwa Joseph. Zikhulupiliro zimenezi zimatitanthauzira kuti ndiye kuti Yesu (A.S) adabadwa munjira yosalongosoka, pomwe ife asilamu tiribe chikhulupiliro chimenechi.

AttachmentSize
File 79a04bbf12b9d808c5e49b71f773d411.mp419.24 MB