Malo omwe Swalat imabwerezedwa

Ndizosatheka kwa munthu pa ntchito za Chipembedzo kumupangira munthu wina? و لا تزر وازرة وزر أخری, koma ngakhale ziri choncho pali malo awiri omwe munthu amatha kumupangira munthu wina ntchito za Chipembedzo monga mwana wamkulu pobweza ma Salat a bambo ake. 1) kumupangira munthu omwalira pa ntchito zokakamizidwa zomwe sadathe kupanga ali moyo. 2) Pantchito za Mustahab, ndi zotheka kuwapangira anthu ena kaya anthuwo akhala kuti adamwalira kapena ali moyo. Monga kuwerenga Quran ndi zina zotero.

AttachmentSize
File 8acb534330b3fd542d6476f3603d68c3.mp46.83 MB