Ntchito zokakamizidwa kupanga mofulumira (Wajib Fawriy)

Pali ntchito zina kuchokera mu ntchito za Chipembedzo zomwe zili zokakamizidwa kwa munthu kuti azipange mofulumira kapena kuti apange zinthuzo nthawi yomweyo pomwe zachitika. Kusiyana ndi ntchito zina zomwe zapatsidwa nthawi yake yaitali. Ndipo dziwani kuti ngati munthu achedwetsa popanga ntchito yofulumirayo ndiye kuti wapanga tchimo.

AttachmentSize
File de2048f048e8385375d4816cdb940b7f.mp411.3 MB