Malamulo oyang\'ana ku Qiblah

Kuyang\'ana ku Qiblah kuli ndi malamulo okwana anayi: 1) Wajib (zokakamizidwa) monga panthawi yomwe munthu akufuna kupemphera, kuzinga nyama ndi… 2) Mustahab, monga panthawi yomwe munthu akudya, kugona, kupanga Duwa ndi…koma kuti zimatengera chitsimikizo cha Munthu. 3) Makrooh, monga panthawi yomwe munthu akukhala malo amodzi ndi mkazi wake (kupanga ukwati). 4) Haram, monga panthawi yopanga chimbudzi (kuyang\'ana kapena kuyang\'anitsa msana).

AttachmentSize
File 930119f3bf27c41d03339325b4941ba9.mp47.86 MB