Manyazi siamapangitsa kuti ntchito za Chipembedzo zisachitike

Mu umoyo watsiku ndi tsiku ngati munthu angapange chinthu chopangaitsa manyazi, ngati chiti chinthucho chiri choletsedwa ndiye kuti kupanga ntchitoyo ndi Haram ndipo ngati ili ya Makrooh ndiye kutinso ntchitoyo ndi Makrooh. Koma ngakhale ziri choncho manyazi omwewo samapangitsa kuti ntchito za chipembedzo zisachitike. Kutanthauza kuti munthu akusiya kupanga lamulo la chipembedzo chifukwa chakuti adachita manyazi. Dziwani kuti zimenezo ndi Haram zoletsedwa.

AttachmentSize
File 8cddfb91c2ba369949cb802b9c0a606d.mp47.76 MB

Add new comment