Kutsutsa Hadith ya \"کتاب الله و سنتی\" \"Bukhu la Mulungu ndi Sunna yanga\"

Hadith imeneyi sikupezeka m\'mabukhu a Ahalsunna. Komanso ma Ulama akulu akulu a Ahalsunna adanena kuti Hadith imeneyi ndi yofooka ndipo adavomereza za Hadith yomwe ikuti \"Bukhu la Mulungu ndi Ahalbait\", komanso kutsatira Hadith imeneyi kuzakhala kusemphana ndi machitidwe a maSheikh akulu akulu a Ahalsunna. Mawunso oti Sunna yanga sakutithetsera ife vuto kapena kutithandiza pofuna kuzindikira chilungamo chifukwa…

AttachmentSize
File 0c418a49a2a776ced025ff2366d5be2b.mp426.61 MB