Kumudziwa Imam Sadiq (A.s) mwachidule (5)

Hadith imeneyi sikupezeka m\'mabukhu a Ahalsunna. Komanso ma Ulama akulu akulu a Ahalsunna adanena kuti Hadith imeneyi ndi yofooka ndipo adavomereza za Hadith yomwe ikuti \"Bukhu la Mulungu ndi Ahalbait\", komanso kutsatira Hadith imeneyi kuzakhala kusemphana ndi machitidwe a maSheikh akulu akulu a Ahalsunna. Mawunso oti Sunna yanga sakutithetsera ife vuto kapena kutithandiza pofuna kuzindikira chilungamo chifukwa…a

AttachmentSize
File 5b7134a96afd4f68bef2b9389af675c9.mp424.22 MB