Kumudziwa Imam Sadiq (A.s) mwachidule (4)

Nthawi zonse Ahalbait (A.S) amakhala akuphedwa chifukwa chakuti mdima ndi omwe umafuna kulamulira ndipo ngati ukufuna kulamulira ukuyenera kuti uchotse kuwala kwina kulikonse ndipo Ahalbait ndi kuwala. Mbiri ina ya Shia ndiko kulimbana ndi anthu opondereza komanso kuwagwira dzanja anthu oponderezedwa komanso kuwateteza ndi kuwathandiza…

AttachmentSize
File 0060e8938014e7d26bdf8e8953c5de31.mp424.22 MB

Add new comment