Ntchito ndi lamulo lake

Ntchito zomwe munthu amagwira zitha kukhala zosangalatsidwa kapenanso zonyasidwa ndi Mulungu. Ndipo ntchito zomwe munthu akupanga zikutuluka kuchokera m\'malamulo asanu (5). Mwachoncho munthu ayenera kudziwa malamulo amanewa ndicholinga choti adzathe kupanga zomwe Mulungu adzasangalala nazo komanso adzathe kusiya zomwe Mulungu amanyasidwa nazo. Malamulo a chipembedzowa ndi awa: 1) Wajib (yokakamizidwa), 2)Haram (choletsedwa), 3) Mustahab (yabwino), 4) Makrooh (yonyasa), 5) Mubah (yololedwa)

AttachmentSize
File 83e4b69b879707541c3d613cd769b548.mp411.16 MB

Add new comment