Khomo la mzinda wa kuzindikira

Ndi zachidzikire kwa aliyense kuti msilamu akuyenera kutsatira munthu yemwe ali ndi kuzindikira konse pa zomwe Mulungu ndi Mtumiki (S.A.A.W) adanena. Osati kutsatira munthu yemwe ali ndi kuzindikira kochipa yemwe nthawi zambiri amalakwitsa m\'malamulo achipembedzo zomwe zidzayambitsa kusokonekera kwa chipembedzo. Mu Hadith ya mtumiki, kudayikidwa kumukonda Ali (A.S) kukhala chizindikiro cha chikhulupiliro ndipo kudana naye ndi chizindikiro cha kukanira. Zonsenzi zikunenedwa ndi mabukhu a Ahalsunna

AttachmentSize
File 71411292509c6ce5e1de15c625048283.mp417.3 MB

Add new comment