Zina zomwe zikutsimikizira pa utsogoleri wa Ali (A.S)

Umar Ibn Khattab akuti: Ali (a.s) ndiye ogemula (Judge) wathu wabwino pakati pa ogemula onse, mtumiki (S.A.A.W) adati: iwe ndi amene udzawalongosolera chilichonse pazinthu zomwe anthu azasemphana maganizo pambuyo pa ine, adatinso Ine ndi mzinda wa maphunziro ndipo Ali (a.s) ndi khomo lake mwachoncho yemwe akufuna kulowa mumzinda wamaphunzirowu adutsire kukhomo…

AttachmentSize
File e24e47142552a9b715ddf94e47d42b05.mp412.66 MB

Add new comment