Ndichifukwa chiyani sindine mkhirisitu?

Chimodzi mwazikhulupiliro za akhirisitu ndiko kunena kuti munthu aliyense ndi ochimwa komanso akubadwa odetsedwa chifukwa cha tchimo lomwe makolo awo (Adam ndi Hawa) adapanga pakudya chipatso ch amtengo oletsedwa. Kodi zimenezi zidzabweretsa vuto lanji?

AttachmentSize
File e0d1466da7ae2d3d49905a6a95d01ff4.mp415.65 MB

Add new comment