Olemekezeka mayi Mariya (S.A) mu Quran – part 1

Inu mayi athu, akazi athu, achimwali athu komanso iwe mtsikana! Kodi mwawayika mayi Maria kukhala chitsanzo chanu pachina chilichonse? Dziwani kuti ngati simukuwatenga mayi Maria kukhala chitsanzo chanu, m'makhalidwe, mukapembedzedwe, kudzisunga komanso mukavalidwe kumene ndiye kuti mukungonama pomatchula dzina la olemekezekawa ndipo palibe chomwe mungapeze chifukwa mudzakhala odedwa kumene ndi Mayiwa.

AttachmentSize
File d7b11b276c85a81160c0805922259186.mp419.59 MB

Add new comment