UBISA ZIKHULUPIRIRO (TAQIYYAH) 1

Chofunikira kudziwa ndichoti Taqiyyah ndi chinthu chomwe nzeru imalamulira. Kodi Taqiyyah ndi chiyani? Kodi Taqiyyah ndiyosiyana ndi bodza, chinyengo, kunama ndi ukamberembere?

AttachmentSize
File 3264d3ded136020d81f80202967f1d2b.mp412.13 MB