Sahaba 1

Swahaba  amapanga zomwe walamulira (fatwa) ndipo ngati angalakwitse ndiye kuti achita Ijtihad ndipo ali ndithawab imodzi. Pachifukwachi tilibe ufulu ofufuza za iwo. Munthu yemwe  angafufuze za kulakwa kwa Swahaba ndikafir.

AttachmentSize
File 2345cdc2c43bff4439ac59153d956a73.mp441.82 MB