Wahabiyyat 2

Chiwahabi chidadzi ndi Muhammad bin Abdul Wahhabi, iyeyu adali ndi zikhulupiriro zodabwitsa kwambiri monga kunena kuti Mtumiki (s.a.w.w)  adali munthu ngati ine mwachoncho inenso nditha kupanga zofanana ndizomwe iye amapanga , ndithanso kukhala Mtumiki.

AttachmentSize
File bf4afeedc6ba7e9f4aa90fabd7e9d0f2.mp432.63 MB