Wahabiyyat 1

Nkhani  yathu ikukhudzana ndi ziwembu zomwe ma Wahabi akuchita mmaiko osiyana siyana.  Ziwembu zomwe angakhale nthawi yaumbuli kudalibe.Nthawi ya umbuli Aluya adali ndi malamulo awo akafuna kumenya nkhondo, amodzi mwa malamulowa ndiko kusamenya nkhondo miyezi ina yolemekezeka monga Muharram. Chisilamu chitafika malamulowa adawavomereza.

AttachmentSize
File 4b4bbd4416f777c28002c8775981e277.mp437.35 MB