Tawassul 1

Koma zomwe mawahhabi akuwanena mashia ndizosemphana ndi Quran mahadith komanso ma sunni chifukwa iwo amakaona manda ama Imam awo monga Abu Hanifa ndi ena. Nawonso mashia amakaona manda ama Imam awo monga Ali, Hasan ndi Husain.

AttachmentSize
File 62bb82e3c175b8d275abac9cbc309e44.mp434.21 MB