Kuonongedwa kwa Quran 5

Kukambirana ndikukokana kwa asilamu pankhaniyi ndikopanda phindu chifukwa choti asilamu amawanena akristu kuti bukhu lawo ndilowonongedwa tsono iwo akamva zimenezi ndiye kuti atengerapo mwayi otinena kuti Quran yathu idaonongedwa.

AttachmentSize
File 68523d1258d72c1c710d74bf58461225.mp49.95 MB