Imam Husain (a.s) part 6

Ndichifukwa chiyani anthu akuKufah sadamuthandize Imam Husain (a.s)
Kukomedwa ndi dziko. Iwo amaona kuti kodi kuli ndalama ndikuti. Anthu okwana 18,000 adabwera ndikugwirana chanza ndi Muslim bin Aqil pomwe okwana 12,000 adamulembea Husain (a.s) makalata oti abwere ku Kufah. Iwo adagwirana chanza ndi Muslim pa 15 Ramadhan ndipo pa 9 dthil hijjah Muslim adaphedwa

AttachmentSize
File 0bc5284abe41a0f5a02c31ea41ffe3bb.mp426.59 MB