Utumiki:Part 20 (A)

Mtumiki (s.a.w.w) samayambitsa nkhondo ayi ndichifukwa chake tikupeza kuti pankhondo zonse zomwe adamenya zokwana 80 kwa zaka 10, anthu omwe adaphedwa ndi 1600, ena akuti 1306 malinga ndi momwe adalembera mu mabuku ena a history.

AttachmentSize
File f1214fc259bd31d70ae2cb3d969a8865.mp418.05 MB

Add new comment