Kusiyana kwa Chiwahhabi ndi Sunni:Gawo 2

Maulawi Abdulrahim (sunni) akunena kuti: “Pakati pa mawahhabi ndi sunni pali kusiyana kwambiri pakuganiza ndizikhulupiriro....Mau anga kwa asilamu asunni anzanga ndi oti mpatuko wachiwahhabi ndiosochera ndipo ukufuna kuononga chisunni choncho musanyengeke

Maulawi Abdulrahim (sunni) akunena kuti: “Pakati pa mawahhabi ndi sunni pali kusiyana kwambiri pakuganiza ndizikhulupiriro....Mau anga kwa asilamu asunni anzanga ndi oti mpatuko wachiwahhabi ndiosochera ndipo ukufuna kuononga chisunni choncho musanyengeke ndi iwo chifukwa choti afalikira mmaiko ambiri.”

AttachmentSize
File 11603-f-chichwa.mp438.55 MB