Kusiyana kwa Chiwahhabi ndi Sunni:Gawo1

Ahlusunnat ali a mipatuko inayi:1- Hannafi 2- Hanbali 3 –Shafi ndi Maliki. Kuchokera mmipatuko imeneyi pakupezekanso mipatuko ina ing’ono ing’ono yomwe ikuchokera mmenemu monga mmpatuko wa chiwahhabi omwe umazinena kuti umatsatira zikhulupiriro za Hanbal

Ahlusunnat  ali a mipatuko inayi:1- Hannafi 2- Hanbali 3 –Shafi ndi Maliki.
Kuchokera mmipatuko imeneyi pakupezekanso mipatuko ina ing’ono ing’ono yomwe ikuchokera mmenemu monga mmpatuko wa chiwahhabi omwe umazinena kuti umatsatira zikhulupiriro za Hanbali.

AttachmentSize
File 11602-f.-chichwa.mp443 MB