Nsichi za Chisilamu

Munthu amene waikira umboni za umodzi wa Mulungu ndi utumiki wa Muhammad ndinso ndikuimika mapemphero, kupereka chopereka, kusala chakudya mmwezi wa Ramadhan ndikupita ku hajji ndi msilamu choncho chuma chake, moyo wake abale ake ndizotetezedwa komanso n

Munthu amene  waikira umboni za umodzi wa Mulungu ndi utumiki wa Muhammad ndinso ndikuimika mapemphero, kupereka chopereka, kusala chakudya mmwezi wa Ramadhan ndikupita ku hajji ndi msilamu choncho chuma chake, moyo wake abale ake ndizotetezedwa komanso ndi olemekezeka kokwanira.

AttachmentSize
File 12017-f-f-chichwa.mp468.31 MB