Zionetsero za Husain (a) mu Quran2.

 

Zionetsero  za  Husain (a)  mu Quran2.
فنظر نظرة فى النجوم * فقال إنى سقي (الصافات / 88 - 89)
Mtumiki  Ibrahim (a)  adayang’ana  nyenyezi  ndipo  adati  Ine  ndikudwala (choncho  sindibwera  nanu  kunsonkhanawo).
Imam  Swadiq (a) zokhudzana  ndi  ayayi  adati: Hazrat  Ibrahim  chifukwa  cha  mavuto  omwe  adzamugwere  Husain (a)  adaganizira  ndikunena  kuti: chifukwa  cha  mavuto omwe  adzamugwere  Husain (a)  ine  ndadwala  nawo.
(Al’awalim:volume 17,tsamba 98)