Zomwe munthu ayenera kudziwa 2

{mp3}audio/bakhsh-audio/317{/mp3}

 

Atsogoleri apambuyo pa mtumiki Muhammad (s.a.a.w) ayenela kukhala anthu osachimwa mu umoyo wawo onse. Qur'an ndi nzeru komanso ma Hadith zikuvomereza pa nkhaniyi.

Add new comment